Fur World

Fur World 🐾Pet Mobile and parlour Grooming
🐾Pet Sitting
🐾Cage Hiring
🐾Dog Walking
🐾Puppy Training
🐾Pet Daycare & boarding
🐾 Dog Photoshoot
🐾Pet nursing
(2)

Good morning and happy new month from Fur World.. Don't forget to subscribe to our grooming packages.  Contact us on 099...
01/08/2026

Good morning and happy new month from Fur World.. Don't forget to subscribe to our grooming packages. Contact us on 0992813337 to learn more.

31/07/2026

Good night from Fur World, mmawa mutipedze ndi galu wanu for a cut and bath. Paja ndi month end komanso weekend. 0992813337.

Zokudya za agalu ndi amphaka komanso modyera agalu available at Fur World. 0992813337 kutalinso timatumiza
31/07/2026

Zokudya za agalu ndi amphaka komanso modyera agalu available at Fur World.
0992813337 kutalinso timatumiza

A very good morning to all our customers.... Tabweretsani galu wanu Lero for grooming, pet day care or boarding...099281...
31/07/2026

A very good morning to all our customers.... Tabweretsani galu wanu Lero for grooming, pet day care or boarding...

0992813337

Tiyeni tigone koma ngati uli pet parent number iyi saver👇0992813337
30/07/2026

Tiyeni tigone koma ngati uli pet parent number iyi saver👇
0992813337

Nayenso The magician amazametesa galu wake ku Fur World... Inu mukuchedwa patipo. Tipedzeni ku Lilongwe area 41 Mkati mw...
30/07/2026

Nayenso The magician amazametesa galu wake ku Fur World... Inu mukuchedwa patipo. Tipedzeni ku Lilongwe area 41 Mkati mwa Peak event garden

Contact us on 0992813337
Thanks Driemo for trusting us with your pet. We are looking forward to visiting us more

Agalu anu sangadye nthawi yabwino ngati chokudyacho Palibe, mapeto Ake mumawagawira chokudya Chanu. Ife a Fur World tili...
30/07/2026

Agalu anu sangadye nthawi yabwino ngati chokudyacho Palibe, mapeto Ake mumawagawira chokudya Chanu.

Ife a Fur World tilinazo zokudya za agalu a misinkhu yonse komanso za amphaka.

Tilankhuleni pa 0992813337 kutalinso timatumidza

See transformation Groomed into this beauty.Book us now... Mobile grooming also available 0992813337
30/07/2026

See transformation
Groomed into this beauty.
Book us now... Mobile grooming also available
0992813337

Good morning from Fur world... Ndi service iti musamaimvesesa ya Fur world tikulongosolereni mmene zimakhalira...
30/07/2026

Good morning from Fur world... Ndi service iti musamaimvesesa ya Fur world tikulongosolereni mmene zimakhalira...

Tikamati pet sitting, timatanthauza kusamalira agalu anu inu mukakhala busy kapena mukatalikira.M***a kumabweretsa mamaw...
29/07/2026

Tikamati pet sitting, timatanthauza kusamalira agalu anu inu mukakhala busy kapena mukatalikira.

M***a kumabweretsa mamawa kuti muzatenge madzulo, kapena kumusiya komkono for a month ndizabwinobwino...

Ife timasamalira
0992813337

Address

Peak Events Garden
Lilongwe
AREA41

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Fur World posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share