Chia Dog Mobile Clinic Lilongwe

Chia Dog Mobile Clinic Lilongwe MUKAFUNA TREATMENT YA AGALU ANU MONGA WADWALA,DEWORMING,MULTIVITAMINS,KUTETEZA KUMATENDA,MANKHWALA A

19/10/2024

Our contacts 0881701347 or 0991292510 both numbers are also on WhatsApp

19/10/2024

If you see signs and symptoms of sickness to your dog, please do not hesitate to contact us.

19/10/2024

Rabies vaccine is available book an appointment with us.

06/10/2024

Good morning, always monitor your dogs if you see any signs of sickness please do not hesitate to contact us. 0881701347 or 0991292510 both numbers also are on WhatsApp.

28/01/2023

Galu Kusosoka Ubweya Sikuti Wadya Nyemba Amakhala Matenda Ife A Chia Dog Clinic Tilinawo Call or watsapp 0881701347 & 0991292510

15/04/2022

Welcome new members

28/01/2022

*DZIWANI ZAMBIRI ZA CHIA DOG MOBILE CLINIC* *(CHIPATALA CHA AGALU CHOYENDAYENDA)*

*1*. *CHIA DOG MOBILE CLINIC IKUPEZEKA KU LILONGWE NDIPO IMAFIKILA PALIPONSE MU LILONGWE MUNO*

*2*.*CHIA DOG MOBILE CLINIC TIMATHANDIZA MATENDA AWA A AGALU
*A*.CHIFUWA CHA AGALU
*B*.NJOKA ZA M'MIMBA
*C*.KUSOSOKA UBWEYA
*D*.KUTSEKULA M'MIMBA
*E*.GALU AKATUPA
*F*.KHANSA YA AGALU
*G*.MANTHONGO NDI MATENDA ENA AMBIRI

*3*.KOMANSO TIMATHENA/KUFULA/CASTRATION AGALU AMUNA
PAMTENGO WA MK10,000

*4*.TIMATSEKA AGALU A AKAZI KUTI ASABEREKE POSACHITA OPERATION PAMTENGO WA MK12,000

*5*, TIMAPEZEKA NDI MANKHWALA AZILONDA ZA AGALU

*6*,TIMABAYA MANKHWALA OTETEZA MATENDA OMWE AMAKONDA KUDWALA AGALU

*7*,TIMABAYA VITAMIN BOOSTER OONJEZERA THANZI LA AGALU ANU

*8*.TIMABAYA KATEMELA OTETEZA KU CHIWEWE( RABIES VACCINE) PAMTENGO WA MK3,000

*9*.NGATI MUKUFUNA THANDIZO LATHU LA MOBILE CLINIC WITHIN LILONGWE TIYIMBIRENI OR WATSAPP # 0881 701 347

Address

Lilongwe

Telephone

+265881701347

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chia Dog Mobile Clinic Lilongwe posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Chia Dog Mobile Clinic Lilongwe:

Share

Category