Mlimi Opambana

Mlimi Opambana Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mlimi Opambana, Lilongwe.
(1)

NZERU ZOPHERA MAKWACHA MU ULIMIThumba limodzi la 50kg NPK kapena UREA kutulutsa matumba 5 a fetereza oti kuthira mbewu z...
08/07/2025

NZERU ZOPHERA MAKWACHA MU ULIMI

Thumba limodzi la 50kg NPK kapena UREA kutulutsa matumba 5 a fetereza oti kuthira mbewu zanu kukolora phwamwamwa.

Pezani book lokongola mukuliona mmchithumzili pa mtengo wa zii muphunzire kupanga nokha ma fertilizer oposa 10 a organic, ma fungicides a organic komanso ma pesticides a organic.

Fee: k3000

Calls / WhatsApp
wa.me/0992644460
wa.me/0886811585

Mukhoza kutijoinaso mu ma training athu a Kalimidwe ka mbewu zosiyanasiyana link mu comment yoyamba.

Thumba limodzi la 50kg NPK kapena UREA kutulutsa matumba 5 a fetereza oti kuthira mbewu zanu kukolora phwamwamwaPezani b...
08/07/2025

Thumba limodzi la 50kg NPK kapena UREA kutulutsa matumba 5 a fetereza oti kuthira mbewu zanu kukolora phwamwamwa

Pezani book lokongola mukuliona mmchithumzili pa mtengo wa zii muphunzire kupanga nokha ma fertilizer oposa 10 a organic, ma fungicides a organic komanso ma pesticides a organic

Fee: k3000

Calls / WhatsApp
0992644460
0886811585

Mukhoza kutijoinaso mu ma training athu a Kalimidwe ka mbewu zosiyanasiyana link mu comment yoyamba

Thumba limodzi la 50kg NPK kapena UREA kutulutsa matumba 5 a fetereza oti kuthira mbewu zanu kukolora phwamwamwa🔘Pezani ...
28/06/2025

Thumba limodzi la 50kg NPK kapena UREA kutulutsa matumba 5 a fetereza oti kuthira mbewu zanu kukolora phwamwamwa

🔘Pezani book lokongola mukuliona mmchithumzili pa mtengo wa zii muphunzire kupanga nokha ma fertilizer oposa 10 a organic, ma fungicides a organic komanso ma pesticides a organic

Fee: k3000

Calls / WhatsApp
0992644460
0886811585

First harvest
16/06/2025

First harvest

Opambana Farmstead
31/05/2025

Opambana Farmstead

*Why should you venture into beans farming right now!?**Pro-Tips* 🇲🇼 Tikunena pano, nyemba pa msika mtengo minimum ndi k...
27/05/2025

*Why should you venture into beans farming right now!?*

*Pro-Tips*

🇲🇼 Tikunena pano, nyemba pa msika mtengo minimum ndi k5000.

🇲🇼Izi zikuthanthauza kuti thumba la 50kg ndi k250, 000.

🇲🇼 Kodi utangokhala ndi matumba 10 ndekuti uli nd makwacha angati?

🇲🇼Chosangalatsa ndi ulimi wa nyemba ndi choti within 3 months m***a kukhala mwakolora. Chinaso mchakuti m***a kulima mwezi wina ulionse. Moti panopa ngati kuthekera kulipo, dzambatukani kalimeni

*Mlimi Opambana*

*Chaka chino kulibe kunamizira kusowa kwa malo*🇲🇼Kodi mukudziwa kuti mbewu zambiri za mgulu la horticulture m***a kulima...
21/05/2025

*Chaka chino kulibe kunamizira kusowa kwa malo*

🇲🇼Kodi mukudziwa kuti mbewu zambiri za mgulu la horticulture m***a kulima mmasaka? Mbewu monga garlic, ginger, Cayenne pepper, tomato, eggplants etc?

*Mlimi Opambana*

Elevate your farming dreams with these simple practical ideas for a small horticultural crop farmer. 0886811585 / 099264...
03/05/2025

Elevate your farming dreams with these simple practical ideas for a small horticultural crop farmer. 0886811585 / 0992644460

23/07/2024

*Available At M-vet🇲🇼*
- Soya full fat @ k1200/kg
- Lime powder k300/kg
- Lime grit k300/kg
- FishMeal k3500/kg
- Molasses k1500/ 500ml
- Sunflower cake k700/kg
- Natural egg booster k8000/pack
- Broiler booster / pack
- Deworming powder. K6000
- Magik powder k8000 big, k4000 small
- Bone meal k4500/kg
- Premix k4500/kg
- Neem powder k5000kg
- Moringa powder k5000/kg
- Limovit k7000

⚫Area 25 Along 49 - Nsungwi

0992644460 / 0886811585

_Even your chicks will recommend M-vet🇲🇼_

22/05/2024

*Available at M-vet Livestock*

Lime /kg
Lime grit /kg
Premix /kg
Moringa /kg
Molasses /kg
Magik powder k4000 & k8000
Broiler booster
Natural deworming powder
Natural egg booster
Fishmeal @ k3500/kg
Neem powder @ k5000/kg
Limovit
Ndi zina zambiri
▪️Located in area 25 along 49-Nsungwi road.

0886811585 / 0992644460

*M-vet Livestock*

18/05/2024

WHAT YOU DIDN'T KNOW ABOUT MOLASSES

⚫Kodi mukudziwapo chani za Molasses?

👉🏿 Muli ma vitamin, potassium, iron komanso calcium zomwe zili zofunika kwambiri ku ziweto zanu maka nkhuku, zinziri, nkhumba, ng'ombe ndi mbuzi.

👉🏿 Molasses mukhoza kupangira broiler booster komaso protease enzyme. Ulimi ndi business.

👉🏿 Molasses amathandiza kupanga improve digestion. Amathandiza kuti chakudya chambiri chizipangidwa convert into meat mmalo mochuluka chitosi.

👉🏿 Ndi anti stress. Amathandiza kubwezeretsa lost minerals and vitamins.

⚫Za ubwino wa molasses tikhoza kuchezera pano

Akupezeka ku M-vet Livestock Solutions ku area 25. K3000 / L

0992644460

*Even the chicks recommend us*

KUPANGA CHAKUDYA CHA ZIWETOKodi ndi zotheka kumapanga feed otchipitsitsa kwambiri ndi mmene zinthu zakwereramu?INDE NDIZ...
18/05/2024

KUPANGA CHAKUDYA CHA ZIWETO

Kodi ndi zotheka kumapanga feed otchipitsitsa kwambiri ndi mmene zinthu zakwereramu?

INDE NDIZOTHEKA TIKUPHUNZITSANI

~Premix muzipanga nokha

~Bone meal, fishmeal, meat meal muzipanga nokha

~Chimanga chanu

~Soya full fat wopanga nokha

~Muziphatikizako leaf meals opanga nokha

In short, kalikose muzipanga nokha

Tumizani mawu okuti add ku number iyi pa WhatsApp +265992644460 muchite nawo maphunziro chaka chino cha 2024. Maphunziro motsogozedwa ndi akadaulo a M-vet Livestock Solutions.

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mlimi Opambana posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share