Ziweto Enterprises Limited

Ziweto Enterprises Limited ZIWETO ENTERPRISE is a network of franchised agro/vet shops providing veterinary solutions for small

Ziweto is a pioneering company building a unique national network of branded retail outlets (6 to date) selling quality livestock inputs, services and training to livestock farmers across Malawi.

28/04/2026

Bambo Kaluwa ndi modzi mwa alimi a Nkhumba mu mzinda wa Mzuzu. Iwowa anayamba ulimiwu mu chaka cha 2023 ndi Nkhumba zazikazi 26 komanso zazimuna 4, koma pakanali pano iwowa alindi ndi Nkhumba zoposa 300 pa farm yawo.

Tiyeni tiwonele video iyi kuti timze zambiri




Empowering Rural Malawi Through Livestock, Enterprise, and OpportunityIn the remote landscapes of northern Malawi, acros...
23/04/2026

Empowering Rural Malawi Through Livestock, Enterprise, and Opportunity

In the remote landscapes of northern Malawi, across Chitipa, Karonga, and Rumphi, a quiet transformation is taking shape. It is driven not by handouts, but by knowledge, enterprise, and a deep understanding of what it takes for rural communities to thrive. At the center of this transformation is Ziweto Enterprises Limited.

As one of Malawi’s leading agribusinesses, Ziweto is redefining how livestock value chains serve smallholder farmers. Through a strategic partnership with Lusubilo Community Care and Catholic Relief Services (CRS), Ziweto is delivering high-impact training programs for Community Animal Health Workers (CAHWs), the frontline providers of animal health services in rural communities.

These trainings go beyond technical instruction. They are designed to build entrepreneurs. CAHWs are equipped with practical skills in livestock health management, alongside essential business capabilities such as drug box management, pricing, and customer service. The result is a new generation of rural service providers who are not only improving animal health but also running sustainable micro-enterprises within their communities.

This initiative is embedded within the Integrated Support for Orphans, Vulnerable Children and Youth 2 (IOVCY 2) project, which uses a graduation model to help vulnerable households transition out of poverty. By enabling families to invest in livestock, the program creates a pathway to income generation, asset building, and resilience. Ziweto’s role ensures that this investment is protected and optimized through access to reliable veterinary services.

The impact is both immediate and systemic. Healthier livestock means higher productivity, more eggs, more meat, more income. Farmers gain confidence in managing their enterprises, while communities benefit from localized access to essential services that were previously distant or unreliable.

Crucially, Ziweto’s support does not end with training. Each CAHW is integrated into Ziweto’s national agrovet network, now spanning 25 shops, creating a direct supply chain for quality veterinary drugs, livestock equipment, and feed. This linkage ensures consistency, trust, and long-term sustainability of services at the community level.

For the CAHWs themselves, the opportunity is transformative. They step into roles as both service providers and entrepreneurs, earning income, building local businesses, and becoming trusted agents of change within their communities.

At its core, this is Ziweto’s philosophy in action: sustainable development is built by strengthening local systems, not bypassing them. By investing in people, knowledge, and market linkages, Ziweto is not just supporting farmers, it is enabling communities to unlock the full value of livestock as a pathway to better livelihoods.

This is how transformation happens. Quietly, locally, and sustainably.

21/04/2026

Mayi Chirambo ndi modzi mwa alimi a Nkhumba mu mzinda wa Mzuzu. Mayiwa anayamba ulimi wa Nkhumba mu chaka cha 2022 ndi Nkhumba ziwiri, koma pakali pano ali ndi Nkhumba zoposa 100. Iwowa amagwiritsa ntchito zakudya za Ziweto komanso mankhwala opezeka ku Ziweto Agrovet Shop.

Tiyeni tiwore video iyi kuti timve zambiri.




Amprolin-300 WSAmprolin-300 WS ndi mankhwala omwe amateteza ziweto zanthu monga Nkhuku, Mbuzi, Nkhosa ndi Ng'ombe  kuti ...
20/04/2026

Amprolin-300 WS

Amprolin-300 WS ndi mankhwala omwe amateteza ziweto zanthu monga Nkhuku, Mbuzi, Nkhosa ndi Ng'ombe kuti zisadwale matenda a kamwanzi (coccidiosis), komanso amachiza thendayi ngati zadwala.

Amagwira ntchito motere:
✅Amateteza kuti ziweto zathu zisadwale nthenda ya kamwazi(coccidiosis) komanso amachiza thendayi ngati zadwala kale
✅Kagwiritsidwe ntchito kake ndikosavuta, timazipasa kudzera mu madzi akumwa
✅Amathana ndi tizilombo tonse toyambitsa matenda akamwazi(Coccidiosis)

📍Akupezeka mu ma shop onse a Ziweto Agrovet

Tiyimbileni:

Chigawo cha Kumpoto: 0997 72 08 63
Chigawo cha Pakati: 0999 83 73 70
Chigawo chakumwela: 0991 07 75 69





Matenda akamwazi ku nkhuku (Coccidiosis)Matenda a kamwazi ku nkhuku (Coccidiosis) ndi oopsa kwambiri chifukwa amachedwet...
13/04/2026

Matenda akamwazi ku nkhuku (Coccidiosis)

Matenda a kamwazi ku nkhuku (Coccidiosis) ndi oopsa kwambiri chifukwa amachedwetsa kukula kwa nkhuku komanso amachepetsa kayikilidwe kake.

Intracox Oral

Intracox ndi mankhwala amphamvu omwe amachiza matenda a kamwazi (Coccidiosis) ku nkhuku.

Amagwira ntchito motere:
✅Amathandiza kuti nkhuku zanu zikhale zathanzi komanso kuti zikule bwino
✅Kagwiritsidwe ntchito kake ndikosavuta, timazipasa kudzera mu madzi akumwa
✅Amathana ndi tizilombo tonse toyambitsa matenda akamwazi (Coccidiosis)

📍Akupezeka mu ma shop onse a Ziweto Agrovet

Tiyimbileni:

Chigawo cha Kumpoto: 0997 72 08 63
Chigawo cha Pakati: 0999 83 73 70
Chigawo chakumwela: 0991 07 75 69





Happy Easter SundayEaster reflects resurrection and renewal, reminding us that even in moments that seem lifeless, there...
05/04/2026

Happy Easter Sunday

Easter reflects resurrection and renewal, reminding us that even in moments that seem lifeless, there is always the power to rise again.

Wishing you a season of new life, growth, and prosperity in your livestock and farming activities, with renewed strength and purpose in all that you do.

04/04/2026

Mayi Janet B Ngwira ndi mm'odzi mwa alimi a Nkhuku za nyama komanso za mazira boma la Ntcheu. Lero akugawana nafe za ubwino wa kuweta Nkhuku pakhomo, komanso akulimbikitsa azimayi anzawo kuti asamangodalira bambo kuti apite ku ntchito kaya ku business. Iwo akuti azimayi nawonso azithamangathamanga poweta Nkhuku pakhomo.

Tiyeni tiwonere video iyi kuti timve zambiri.

Dear valued customersPlease take note of our shop operating schedule during the Easter holiday period to help you plan y...
02/04/2026

Dear valued customers

Please take note of our shop operating schedule during the Easter holiday period to help you plan your purchases in advance.

We encourage you to buy early to avoid last-minute inconvenience.

Thank you for your continued support, and we wish you a joyful and blessed Easter!

30/03/2026
30/03/2026

Bambo Aron Chijana Banda ndi bambo Dzinkambani Sitolo ndi alimi a nkhuku za mazila ku Mponela mu boma la Dowa. Awiriwa akufotokoza momwe Ziweto feed ndi mankhwala osiyanasiyana opezeka ku Ziweto Agrovet Shop awapindulira pa ulimi wawo wa nkhuku.

Imvani zambiri mu video iyi.

Zipangizo za ulimi wa ziweto zapamwambaZaguleni zipangizo za pamwamba zogwiritsa ntchito pa ulimi wanu wa ziweto. Zipang...
25/03/2026

Zipangizo za ulimi wa ziweto zapamwamba

Zaguleni zipangizo za pamwamba zogwiritsa ntchito pa ulimi wanu wa ziweto. Zipangizo monga, ma sprayer, ndolo za ng'ombe ndi mbuzi komanso ma syringes a automatic ndi zina zambiri ku ma Shop a Ziweto Agrovet.

Chidziwitso chapaderaOkondedwa ma kasitomala athu, muli kudziwitsidwa kuti pa 23rd March 2026 lomwe ndi tsiku la tchuthi...
20/03/2026

Chidziwitso chapadera

Okondedwa ma kasitomala athu, muli kudziwitsidwa kuti pa 23rd March 2026 lomwe ndi tsiku la tchuthi cha Eid, ma shop athu a Ziweto Agrovet azakhala otsekula kuyambila 8AM kulekeza 2PM.

Zikomo.

Address

Malangalanga
Lilongwe

Opening Hours

Monday 08:00 - 17:00
Tuesday 08:00 - 17:00
Wednesday 08:00 - 17:00
Thursday 08:00 - 17:00
Friday 08:00 - 17:00
Saturday 08:00 - 14:00

Telephone

+265996148029

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ziweto Enterprises Limited posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Ziweto Enterprises Limited:

Share